Winamp Logo
Tisanthule Baibulo @ ttb.twr.org/chichewa Cover
Tisanthule Baibulo @ ttb.twr.org/chichewa Profile

Tisanthule Baibulo @ ttb.twr.org/chichewa

English, Religion, 1 season, 389 episodes, 8 hours, 57 minutes
About
Pologalamu ya Tisanthule Baibulo ndi gawo limodzi lautumiki, ophunzitsa Baibulo, otchedwa ulendo m??baibulo (Thru the Bible). Mndandanda wamapogalamuwu unakonzedwa ndi Dr. J. Vernon McGee ndipo unatanthauzidwa mu zilankhulo zoposa zana zimodzi (100). Zinakonzedwa kuti pologalamu imodzi idzikhala ya mphindi makumi atatu (30) ndipo kuti pomaliza zidzathe kuthandiza omvera kumvetsetsa Baibulo lonse. Ndipo pakali pano mapologalamu onsewa tawaika pamakina a Intaneti. Ndife oyamika kuti mwasankha kuphunzira zambiri zokhudza mau a Mulungu kudzera mmapologalamuwa. Tikukulimbikitsani kuti mudzimvera pologalamu imodzi patsiku kuyambira lolemba mpaka lachisanu. Ngati mungakwanitse kutsatira ndondomekoyi, pakutha kwa zaka zisanu mudzakhala kuti mwawerenga Baibulo lonse.
Episode Artwork

Yetulo ayendera Mose

1/1/128 minutes, 33 seconds
Episode Artwork

Anthu asankha lamulo mmalo mwa chisomo

1/1/127 minutes, 53 seconds
Episode Artwork

Malamulo Khumi

1/1/128 minutes, 30 seconds
Episode Artwork

Malamulo paukapolo ndi kupwetekana

1/1/128 minutes, 27 seconds
Episode Artwork

Malamulo okhudza magulu a anthu ndi katundu

1/1/128 minutes, 4 seconds
Episode Artwork

Mose paphiri la Sinayi

1/1/127 minutes, 48 seconds
Episode Artwork

Likasa ndi Chotetezerapo

1/1/129 minutes, 4 seconds
Episode Artwork

Zipangizo Zopezeka Mkati Mwa Chipinda Cha Kunja Kwa Kachisi Ndi Kufunika Kwake

1/1/128 minutes, 32 seconds
Episode Artwork

Zobvala Za Wa Nsembe Wamkulu Amene Ayimira Yesu

1/1/129 minutes, 24 seconds
Episode Artwork

Gome La Mkate Woonekera, Choyikapo Nyali Ndi Nsaru Zophimba

1/1/129 minutes, 3 seconds
Episode Artwork

Kupembeza

1/1/127 minutes, 21 seconds
Episode Artwork

Kupatulika Kwa Aroni Ndi Ana Ake Ku Ntchito Ya Mulungu

1/1/127 minutes, 53 seconds
Episode Artwork

Pakuthana Ndi Uchimo Pamakhalanso Chiyanjano Ndi Mulungu

1/1/130 minutes, 15 seconds
Episode Artwork

Mphatso Zapadera, Tsiku La Sabata Ndi Mwana Wa Ng’ombe Woumba

1/1/128 minutes, 59 seconds
Episode Artwork

Mulungu Akupitilizabe Kukozekeretsa Anthu Za Dziko La Malonjezano

1/1/127 minutes, 42 seconds
Episode Artwork

Zithunzi Za Yesu Khristu Mkachisi

1/1/127 minutes, 38 seconds
Episode Artwork

Zovala Za Wa Nsembe Wamkulu Zimaonetsa Ulemerero Wa Mulungu

1/1/129 minutes, 47 seconds
Episode Artwork

Njira Ya Chipulumutso Yikuonekera M’kachisi

1/1/126 minutes, 57 seconds
Episode Artwork

Yesu Mtumiki Wa Mulungu

1/1/128 minutes
Episode Artwork

Chiyambi Cha Bukhu La Mariko Komanso Chiyambi Chakuona Za Mtumiki

1/1/128 minutes, 53 seconds
Episode Artwork

Mtumiki Wa Mulungu Wayamba Ntchito

1/1/128 minutes, 15 seconds
Episode Artwork

Yesu Mtumiki Athetsa Nzeru Gulu La Anthu

1/1/128 minutes, 53 seconds
Episode Artwork

Kupitiliza Kuona Ntchito Ya Yesu

1/1/128 minutes, 42 seconds
Episode Artwork

Yesu Apitiliza Kuonetsa Zozizwa Zoonetsa Kuti Ntchito Yachitika

1/1/129 minutes, 1 second
Episode Artwork

Yesu Aphunzitsa Kupyolera M’mafanizo Oonetsa Ntchito

1/1/127 minutes, 41 seconds
Episode Artwork

Yesu Ali Paulendo Wopita Kokaphedwa

1/1/127 minutes, 44 seconds
Episode Artwork

Yesu Achita Chifuniro Cha Mulungu

1/1/126 minutes, 56 seconds
Episode Artwork

Utumiki Wa Yesu Ufika Pachimake

1/1/128 minutes, 47 seconds
Episode Artwork

Yesu Aoneka Ndi Maonekedwe Yonyezimila Pa Phiri

1/1/127 minutes, 47 seconds
Episode Artwork

Yesu Akwera Ku Yerusalemu

1/1/128 minutes, 16 seconds
Episode Artwork

Yesu Ayesedwa

1/1/129 minutes, 5 seconds
Episode Artwork

Kumaliza Kwa Utumiki Wa Yesu Padziko Lapansi Pano

1/1/127 minutes, 33 seconds
Episode Artwork

Chiphunzitso Cha Paphiri La Oliveti- Zisonyezo Za Kutha Kwa Nyengo

1/1/128 minutes, 1 second
Episode Artwork

Yesu Ali Panjira Yokapachikidwa

1/1/127 minutes, 45 seconds
Episode Artwork

Mgwirizano Wodabwitsa Pakati Pa Kumwamba Ndi Gehena

1/1/127 minutes, 59 seconds
Episode Artwork

Yesu Aperekedwa Nsembe

1/1/128 minutes, 20 seconds
Episode Artwork

Yesu Auka Kwa Akufa Ndi Kukwera Kumwamba

1/1/127 minutes, 58 seconds
Episode Artwork

Chiyambi Cha Bukhu La Levitiko Ndi Za Nsembe Yopsereza

1/1/127 minutes, 37 seconds
Episode Artwork

Nsembe Ya Ufa Ndi Ya Zipatso Zoyamba

1/1/128 minutes, 10 seconds
Episode Artwork

Malamulo, Mwambo Ndi Chifukwa Chopereka Yopsereza

1/1/127 minutes, 33 seconds
Episode Artwork

Nsembe Ya Mtendere

1/1/126 minutes, 25 seconds
Episode Artwork

Nsembe Ya Uchimo Pochimwa Wansembe

1/1/127 minutes, 59 seconds
Episode Artwork

Kuunika Za Nsembe Yopalamula

1/1/129 minutes, 34 seconds
Episode Artwork

Zochimwa Za Mtundu Wonse Wa Israyeli, Mtsogoleri Ndi Anthu Wamba

1/1/127 minutes, 21 seconds
Episode Artwork

Nsembe Yopalamula Ndi Nsembe Ya Mtendere

1/1/128 minutes, 7 seconds
Episode Artwork

Kupatulika Kwa Ansembe

1/1/127 minutes, 35 seconds
Episode Artwork

Ntchito Ya Tsiku Ndi Tsiku Ya Ansembe

1/1/126 minutes, 43 seconds
Episode Artwork

Chakudya Cha Anthu A Mulungu

1/1/128 minutes, 13 seconds
Episode Artwork

Nyama Zodetsedwa Ndi Zosadetsedwa

1/1/127 minutes, 4 seconds
Episode Artwork

Mulungu Athana Ndi Kugalukira Ndi Kusamvera

1/1/127 minutes, 17 seconds
Episode Artwork

Kutengera Uchimo Kuchokera Kwa Makolo Kapena Kuti Kupatsirana Machimo Kuchokera Kwa Makolo

1/1/128 minutes, 8 seconds
Episode Artwork

Tikambirana Za Nthenda Ya Khate

1/1/126 minutes, 23 seconds
Episode Artwork

Kupitiliza Kuona Nkhani Ya Khate

1/1/127 minutes, 10 seconds
Episode Artwork

Mwambo Woyeretsa Munthu Wakhate

1/1/125 minutes, 32 seconds
Episode Artwork

Mabala Akukha Kapena Mabala Otuluka Magazi

1/1/126 minutes, 55 seconds
Episode Artwork

Kuunika Zo Ukha

1/1/127 minutes, 22 seconds
Episode Artwork

Tsiku Lotetezera

1/1/127 minutes, 26 seconds
Episode Artwork

Pali Malo Amodzi Operekera Nsembe

1/1/127 minutes, 43 seconds
Episode Artwork

Makhalidwe Oyenera Ya Ana Amulungu

1/1/127 minutes, 20 seconds
Episode Artwork

Ubale Wa Munthu

1/1/127 minutes, 18 seconds
Episode Artwork

Chilango Cha Kupha

1/1/127 minutes, 45 seconds
Episode Artwork

Kudetsedwa Kwa Unsembe Ndi Maliro

1/1/127 minutes, 53 seconds
Episode Artwork

Nyengo Kapena Nthawi Yopatulika

1/1/127 minutes, 39 seconds
Episode Artwork

Kupitiliza Kuona Za Nyengo Yopatulika

1/1/127 minutes, 41 seconds
Episode Artwork

Choyikapo Nyali Ndi Mkate Woonekera

1/1/126 minutes, 48 seconds
Episode Artwork

Chaka Chopuma Ndi Chaka Chachikondwerero

1/1/128 minutes, 42 seconds
Episode Artwork

Tsogolo La Mtundu Wa Israyeli

1/1/127 minutes, 54 seconds
Episode Artwork

Kugwiritsa Ntchito Pangano

1/1/129 minutes, 48 seconds
Episode Artwork

Chiyambi Ndi Kuonetsa Cholinga Cha Bukhuli

1/1/129 minutes, 35 seconds
Episode Artwork

Kulengeza Kwa M’ngelo Gabrieli

1/1/128 minutes, 28 seconds
Episode Artwork

Nyimbo Za Khisimisi

1/1/127 minutes, 25 seconds
Episode Artwork

Zinthu Zomwe Zinachitika Kwa Mariya

1/1/128 minutes, 31 seconds
Episode Artwork

Simeoni Ndi Anna Azindikira Mesiya; M’nyamata Yesu Ali M’kachisi; Kuyambika Kwa Utumiki Wa Yohane

1/1/128 minutes, 3 seconds
Episode Artwork

Yohane M’batizi; Kuunika Muzu WaMariya, Komanso Kuyesedwa Kwa Yesu

1/1/129 minutes, 50 seconds
Episode Artwork

Yesu Akanidwa Ndi Abale Wake

1/1/127 minutes, 32 seconds
Episode Artwork

Yesu Asankha Ophunzira, Achiritsa Ndi Kuphunzitsa

1/1/129 minutes, 52 seconds
Episode Artwork

Kusankha Ophunzira Khumi Ndi Awiri Ndi Chiphunzitso Chapachigwa

1/1/126 minutes, 32 seconds
Episode Artwork

Machilitso, Kuukitsa Akufa Ndi Kuyamikira Yohane M’batizi

1/1/127 minutes
Episode Artwork

Yesu Aphunzitsa Kudzera M’mafanizo

1/1/127 minutes, 50 seconds
Episode Artwork

Mose Apereka Ndi Kumasuliranso Malamulo

1/1/126 minutes, 52 seconds
Episode Artwork

Chikondi Cha Mulungu Chionekera Mwa Isarayeli Ndipo Ayenera Kuphunzitsa Ana Kupembedza Mulungu M’mzimu

1/1/126 minutes
Episode Artwork

Ulendo Wa Yesu Ku Yerusalemu

1/1/127 minutes, 6 seconds
Episode Artwork

Fanizo La Msamariya Wachifundo

1/1/127 minutes, 16 seconds
Episode Artwork

Yesu Aphunzitsa Za Pemphero Komanso Adzudzula Afarisi

1/1/128 minutes, 34 seconds
Episode Artwork

Yesu Aphunzitsa Ndi Mafanizo Ambiri

1/1/126 minutes, 56 seconds
Episode Artwork

Yesu Akupitiliza Kuphunzitsa Ndi Kuchilitsa Pa Ulendo Waku Yerusalemu

1/1/127 minutes, 51 seconds
Episode Artwork

Yesu Aphunzitsa Kudzera M’mafanizo Osiyana-Siyana

1/1/127 minutes, 2 seconds
Episode Artwork

Yesu Akuphunzitsa Kudzera M’mafanizo A Nkhosa Yosokera, Ndalama Yotayika, Ndi Wana Awiri Wolowerera

1/1/129 minutes, 12 seconds
Episode Artwork

Fanizo La Kapitawo Wonyenga Ndi Yankho La Yesu Kwa Afarisi

1/1/125 minutes, 58 seconds
Episode Artwork

Yesu Alangiza Wophunzira Onse

1/1/128 minutes, 56 seconds
Episode Artwork

Yesu Alirira Mzinda Wa Yerusalemu

1/1/128 minutes, 26 seconds
Episode Artwork

Yesu Aphunzitsa Kupyolera M’mafanizo Osiyana Siyana Komanso Adalitsa Wana

1/1/126 minutes, 15 seconds
Episode Artwork

Yesu Akufunsidwa Za Ulamuliro Wake Ndipo Yesu Akuwayankha

1/1/128 minutes, 36 seconds
Episode Artwork

Yesu Ayankha Funso Lakuti Kodi Zinthu Izi Zidzaoneka Liti?

1/1/128 minutes, 51 seconds
Episode Artwork

Zochitika Zomwe Zikuonetsa Kumalizika Kwa Utumiki Wa Yesu

1/1/128 minutes, 47 seconds
Episode Artwork

Amgwira Yesu Ndipo Apita Naye Kumabwalo Ya Mirandu

1/1/128 minutes, 23 seconds
Episode Artwork

Yesu Achoka Kubwalo La Milandu Kupita Kukapachikidwa

1/1/128 minutes, 14 seconds
Episode Artwork

Yesu Ayikidwa M’manda Ndi Kuuka Kwa Akufa

1/1/129 minutes, 44 seconds
Episode Artwork

Yesu Adziwonetsa Kwa Anthu Ambiri Ndi Kukwera Kumwamba

1/1/126 minutes, 33 seconds
Episode Artwork

Chiyambi Cha Bukhu Ndi Kuwerengedwa Kwa Ana A Israyeli

1/1/128 minutes, 49 seconds
Episode Artwork

Mtsitsi Kapena Muzu Wa Ana A Israyeli Ndi Kakhalidwe Kadongosolo Ka Pa Chigono

1/1/124 minutes, 49 seconds
Episode Artwork

Pfuko La Alevi Pamodzi Ndi Ntchito Yawo, Lipatsidwa Kwa Wansembe Wamkulu

1/1/124 minutes, 6 seconds
Episode Artwork

Kudetsedwa Kudzera Mwa Nthenda Ndi Uchimo

1/1/127 minutes, 38 seconds
Episode Artwork

Kufunika Kwa Lumbiro La Unanziri Ndi Madalitso Autatu Wa Mulungu Ndi mphatso zake

1/1/125 minutes, 12 seconds
Episode Artwork

Kuwala Kuchokera Kuchoyikapo Nyali, Alevi Ayeretsedwa, Paskha Ndi Kutsogoleredwa Kwa Israyeli

1/1/126 minutes, 52 seconds
Episode Artwork

Malipenga A Siliver, Mpongozi Wa Mose Ndipo A Israyeli Ayamba Kuyenda Ndipo Adandaula

1/1/125 minutes, 25 seconds
Episode Artwork

Mana, Mose Adandaula, Mulungu

1/1/128 minutes
Episode Artwork

Mose Atuma Akazonde, Israyeli Sakukhulupilira Mulungu, Chilango Cha Mulungu Ndi Kulapa Kwa Israyeli

1/1/124 minutes, 49 seconds
Episode Artwork

Kuunikanso Kuti Chikonzero Cha Yehova Sichidaonongeke, Chilango Cha Imfa Posasunga Sabata, Kuukira Kwa Kora

1/1/126 minutes, 46 seconds
Episode Artwork

Kuukira Kwa Kukulu Ndikutsatira Chilango Chachikulu, Komanso Kuukanso Kwa Aroni

1/1/125 minutes, 24 seconds
Episode Artwork

Aroni Ndi Alevi Akhazikitsidwa Pa Ntchito Yawo, Ndi Kuunika Udindo Wawo

1/1/126 minutes, 10 seconds
Episode Artwork

Kudandaula Pa Kadeshi, Madzi Aturuka

1/1/126 minutes, 37 seconds
Episode Artwork

Chigonjetso Cha A Israyeli, Kudandaula Kwa Chisanu Ndi Chitatu, Njoka Ya Mkuwa, Nyimbo Yachiyamiko Ndi Za Balak Ndi Balaamu

1/1/125 minutes, 20 seconds
Episode Artwork

Balaki Afuna Baalamu Kuti Atemberere Israyeli, Koma Baalamu Adalitsa Israyeli

1/1/126 minutes, 40 seconds
Episode Artwork

Ulosi Wachinayi, Nzeru Ya Balamu Ndi Chiwerengero Cha M’badwo Watsopano

1/1/128 minutes, 59 seconds
Episode Artwork

Cholowa Cha Wana Wa Akazi, Mose Akonzekera Kufa, Zopereka Ndi Kulambira Koona

1/1/125 minutes, 30 seconds
Episode Artwork

Kupitiliza Kuona Za Lamulo La Kaperekedwe Ka Nsembe, Ndi Malumbiro

1/1/127 minutes, 33 seconds
Episode Artwork

Chilango Cha Amidyani, Rubeni Ndi Gadi Afuna Dziko Lawo, lamulo La Kutenga Dziko, Malire A Dziko Lamalonjezano, Midzi Ya Alevi Ndi Lamulo Lacholowa

1/1/127 minutes, 37 seconds
Episode Artwork

Mau Auuluridwa /Afotokonzeredwa

1/1/129 minutes, 44 seconds
Episode Artwork

Umunthu Wa Mwana Wa Mulungu

1/1/128 minutes, 37 seconds
Episode Artwork

Umboni Wochitira Yesu Wa Anthu Anayi

1/1/128 minutes, 14 seconds
Episode Artwork

Ntchito Yoyamba Ya Yesu Pa Ukwati Wa Ku Kana

1/1/125 minutes, 45 seconds
Episode Artwork

Yesu Agwiritsa Ntchito Mau Poyeretsa Kachisi Ndi Nkhani Ya Nikodemo

1/1/128 minutes, 16 seconds
Episode Artwork

Ulendo Wa Nikodemo Ndi Umboni Wa Yohane M’batizi

1/1/126 minutes, 28 seconds
Episode Artwork

Yesu Akumana Ndi Mkazi Pa Chitsime

1/1/126 minutes, 20 seconds
Episode Artwork

Chipulumutso M’mudzi Wa Samariya

1/1/125 minutes, 38 seconds
Episode Artwork

Yesu Aulura Umulungu Wake Ndipo Ayuda Atsutsana Naye

1/1/125 minutes, 21 seconds
Episode Artwork

Yesu Atsimikiza Kunena Kuti Iye Ndi Atate Wake, Ali Amodzi

1/1/125 minutes, 13 seconds
Episode Artwork

Yesu Adyetsa Anthu Zikwi Zisanu (5,000) Komanso Ayenda Pa Nyanja

1/1/126 minutes, 44 seconds
Episode Artwork

Yesu Apitiliza Kuphunzitsa Za Mkate Wamoyo

1/1/126 minutes, 9 seconds
Episode Artwork

Yesu Adziulula Kuti Ndiye Mkate Wa moyo

1/1/124 minutes, 54 seconds
Episode Artwork

Udani Ukukula Pa Yesu

1/1/127 minutes, 13 seconds
Episode Artwork

Yesu Akhulukira Mkazi Wogwidwa Chigololo

1/1/127 minutes, 45 seconds
Episode Artwork

Yesu Akudziulura Kuti Ndiye Kuunika Kwa Dziko Lapansi

1/1/125 minutes, 23 seconds
Episode Artwork

Yesu Atsegula Maso A Munthu Amene Anabadwa Ali Wakhungu

1/1/126 minutes, 23 seconds
Episode Artwork

Munthu Wosaona Uja, Tsopano Waona Yesu

1/1/125 minutes, 41 seconds
Episode Artwork

Israyeli Akuonetsa Chithunzi Chakuti Ndikhola La Nkhosa

1/1/126 minutes, 17 seconds
Episode Artwork

Yesu Akudziula Kuti Ndiye M’busa Wabwino

1/1/129 minutes, 13 seconds
Episode Artwork

Yesu Akonzekeretsa Ophunzira Wake Kuti Akumane Ndi Lazaro

1/1/126 minutes, 34 seconds
Episode Artwork

Yesu Aukitsa Lazaro Kwa Akufa

1/1/125 minutes, 43 seconds
Episode Artwork

M’yuda Ndi Ahelene Achitira Yesu Umboni

1/1/125 minutes, 57 seconds
Episode Artwork

Yesu Alowa M’nthawi Ya Masautso

1/1/128 minutes, 18 seconds
Episode Artwork

Yesu Asambitsa Mapazi Ya Ophunzira Ake

1/1/127 minutes, 40 seconds
Episode Artwork

Yudase Achoka Ndipo Yesu Aneneratu Kuti Petro Adzamukana Iye

1/1/125 minutes, 57 seconds
Episode Artwork

Yesu Alimbikitsa Ophunzira Wake

1/1/128 minutes, 12 seconds
Episode Artwork

Yesu Alonjeza Mzimu Woyera

1/1/126 minutes, 41 seconds
Episode Artwork

Yesu Adzitchula Kukhala Mpesa Ndipo Ophunzira Ake Ndiwo Nthambi

1/1/127 minutes, 45 seconds
Episode Artwork

Wophunzira Ayenera Kukhala Mwa Yesu Ndi Kumumvera Iye

1/1/125 minutes, 42 seconds
Episode Artwork

Yesu Achenjeza Za Kubwera Kwa Otsutsa

1/1/129 minutes, 13 seconds
Episode Artwork

Kupitiliza Kuphunzitsa Za Mzimu Woyera

1/1/129 minutes, 5 seconds
Episode Artwork

Yesu Apenya Mtsogolo Ndi Chiyembekezo Cha Mtanda

1/1/129 minutes, 42 seconds
Episode Artwork

Yesu Apempherera Ophunzira Wake M’nyengo Yonse

1/1/128 minutes, 32 seconds
Episode Artwork

Yesu Agwidwa M’munda Wa Getsemane

1/1/128 minutes, 5 seconds
Episode Artwork

Midzi Ya A Levi Ndi Midzi Iwiri Ya Hafu Ikhala Kum’mawa Kwa Yordano

1/1/126 minutes, 54 seconds
Episode Artwork

Yesu Kubwalo La Annasi Ndi Pilato

1/1/128 minutes, 13 seconds
Episode Artwork

Imfa Ya Yesu Pa Mtanda

1/1/128 minutes, 40 seconds
Episode Artwork

Kuuka Ku Manda Kwa Yesu Kristu

1/1/128 minutes, 16 seconds
Episode Artwork

Ophunzira Aona Yesu Atauka Kumanda

1/1/129 minutes, 4 seconds
Episode Artwork

Mau Omaliza A Yohane Otseka Nawo Bukhu

1/1/128 minutes, 46 seconds
Episode Artwork

Chiyambi Cha Bukhu La Deuterenomo Ndi Kuona Za Uchimo WaIsrayeli Pa Kadesi Barnea

1/1/127 minutes, 28 seconds
Episode Artwork

Mose Aunikanso Za Kulephera Kwa Israyeli M’njira Zosiyana-Siyana Ndipo awalimbikitsa Kuti Amvere Mulungu

1/1/125 minutes
Episode Artwork

Chipulumutso Ndiubale Omwe

1/1/127 minutes, 27 seconds
Episode Artwork

Zomwe Anachita Mulungu M’mbuyomo, Ndizimene Zimapereka Chilimbikitso Pa Zomwe Mulungu Adzachite

1/1/125 minutes, 11 seconds
Episode Artwork

Lamulo Lakutenga Malo, Malo Amodzi Opembedzerapo, Malamulo A Zakudya Ndi Kuchenjeza Za Aneneri Onama

1/1/128 minutes, 6 seconds
Episode Artwork

Kulephera Kwa Israyeli; Miyala Ya Malamulo Atsopano; Kupembedzera Kwa Mose; Kupatulidwa Kwa A Levi; Chisamaliro Cha Mulungu; Ndi Lamulo La Kutenga Malo

1/1/127 minutes, 16 seconds
Episode Artwork

Kupitiliza Za Aneneri Onama; Midzi Yonyasa; Chikhalidwe Ndi malamulo apa Chakudya ndi chakhumi

1/1/127 minutes, 11 seconds
Episode Artwork

Chaka Chopuma, Ukapolo, Madyerero Atatu, Kuweruza Ndi Kupembedza Mafano

1/1/128 minutes, 42 seconds
Episode Artwork

Kumtumikira Mulungu Ndi Mtima Wonse;

1/1/130 minutes, 22 seconds
Episode Artwork

Mesiya, Mneneri Woona Ndi Onama, Midzi Yopulumikira Ndi Malamulo Wena

1/1/129 minutes
Episode Artwork

Malamulo A Nkhondo, Kupha, Amayi

1/1/128 minutes, 40 seconds
Episode Artwork

Chilango Chopachikidwa Pamtengo; Za

1/1/127 minutes, 35 seconds
Episode Artwork

Kukhala Mu Israyeli, Ukhondo, Malamulo A Mose Pa Kuthetsa Ukwati Ndi Malamulo Wena

1/1/127 minutes, 45 seconds
Episode Artwork

Malonjezo A Mulungu; Madalitso Pakumvera Ndi Tsoka Pa kusamvera

1/1/127 minutes, 34 seconds
Episode Artwork

Kukwapula Wolakwa, Kuteteza Mkazi Wamasiye, Chilango Cha Amaleke, Ndi Chopereka Cha Zipatso Zoyamba

1/1/127 minutes, 52 seconds
Episode Artwork

Pangano La Dziko La Malonjezano

1/1/127 minutes, 44 seconds
Episode Artwork

Moyo Ndi Zabwino Kulinganiza Ndi Imfa Ndi Zoyipa; Kusintha Kwa Utsogoleri

1/1/128 minutes, 22 seconds
Episode Artwork

Nyimbo Ya Mose, Mdalitso Ndi Imfa Yake Ulamuliro Wake

1/1/129 minutes, 9 seconds
Episode Artwork

Chiyambi Cha Bukhu La Yoswa, Yoswa Atenga Udindo Ndi

1/1/128 minutes, 28 seconds
Episode Artwork

Yoswa Atenga Ulamuliro Pa Israyeli

1/1/127 minutes, 17 seconds
Episode Artwork

Israyeli Aoloka Mtsinje Wa Yordano

1/1/127 minutes, 59 seconds
Episode Artwork

Zinthu Zitatu Zochitika Komanso Zofunika Kwambiri

1/1/126 minutes, 36 seconds
Episode Artwork

Kugonjetsa Mudzi Wa Yeriko

1/1/125 minutes, 47 seconds
Episode Artwork

Israyeli Alephera kugonjetsa Ai Kenaka Tiona Kupasuka kwake

1/1/127 minutes, 11 seconds
Episode Artwork

A Gibeoni Ndi Nkhondo Yochokera Kum’mwera

1/1/126 minutes, 4 seconds
Episode Artwork

Kutsiriza Nkhondo Ya Kum’mwera Ndi Kupita Kumpoto Kwa Kanani

1/1/125 minutes, 40 seconds
Episode Artwork

Dziko La Kum’mawa Kwa Mtsinje Wa Yordano Ndi Gawo La Kalebe

1/1/126 minutes, 1 second
Episode Artwork

Kudula Malire A Malo A Mapfuko Ya Ana A Israyeli

1/1/126 minutes, 21 seconds
Episode Artwork

Kumaliza Kugawa Madera Kwa Ana A Israyeli Ndi Midzi Yopulumukiramo

1/1/126 minutes, 14 seconds
Episode Artwork

Uthenga womaliza wa Yoshuwa

1/1/128 minutes, 55 seconds
Episode Artwork

Zochitika ku Israyeli atamwalira Yoshua

1/1/126 minutes, 5 seconds
Episode Artwork

Nyimbo ya Debora ndi Baraki

1/1/128 minutes, 27 seconds
Episode Artwork

Mulungu agwiritsa anthu wamba kupulumutsa Israyeli

1/1/127 minutes
Episode Artwork

Kulowelera kwa kachisanu ndi chimodzi

1/1/126 minutes, 47 seconds
Episode Artwork

Mulungu apulumutsa Israyeli kudzera mwa Gidiyoni

1/1/127 minutes, 48 seconds
Episode Artwork

Zaka 40 zamtendere pansi pa utsogoleri wa Gidiyoni

1/1/127 minutes, 43 seconds
Episode Artwork

Utsogoleri wakanika

1/1/126 minutes, 53 seconds
Episode Artwork

Nsanje ya Efurayimu, za oweruza ena anatu

1/1/128 minutes, 7 seconds
Episode Artwork

Yefuta abweretsa chipambano kwa Amoni

1/1/127 minutes, 59 seconds
Episode Artwork

Oweruza Samusoni

1/1/126 minutes, 48 seconds
Episode Artwork

Dziko lilowerera pauzimu ndi pa ndale

1/1/128 minutes, 30 seconds
Episode Artwork

Chiyambi, Kulowa ku Moabu

1/1/129 minutes, 40 seconds
Episode Artwork

Kubwerera ku Betelehemu

1/1/126 minutes, 32 seconds
Episode Artwork

Rute Akunkha Chakudya M’munda Wa Boazi

1/1/127 minutes, 14 seconds
Episode Artwork

Rute Apitiliza Kukunkha Chakudya M’munda Wa Boazi

1/1/127 minutes, 24 seconds
Episode Artwork

Rute kukunkha kwa Boazi

1/1/126 minutes, 53 seconds
Episode Artwork

Rute asankha Boazi ngati mlowamalo

1/1/127 minutes, 7 seconds
Episode Artwork

Rute mumtima komanso pakhomo la Boazi

1/1/128 minutes, 20 seconds
Episode Artwork

Mlatho komanso Mbiri ya bukhu

1/1/128 minutes, 13 seconds
Episode Artwork

Yesu alangiza Ophunzira ake, alonjeza mzimu woyera komanso za kukwera kwake

1/1/125 minutes, 37 seconds
Episode Artwork

Kuyamba kwa mpingo komanso ubatizo wa Mzimu Woyera

1/1/127 minutes, 33 seconds
Episode Artwork

Petulo ayankha otsutsana naye, Uneneri wa Yoeli; Petulo alalika Yesu anthu 3,000 nkutembenuka mtima

1/1/127 minutes, 31 seconds
Episode Artwork

Mphamvu za Mzimu Woyera, Petulo alalikiranso

1/1/128 minutes, 3 seconds
Episode Artwork

Kusakondwa Kwa Atsogoleri A Chiyuda Ndi Petro Ndi Yohane; Kuweruza Kwachilendo; Kuopseza;

1/1/126 minutes, 56 seconds
Episode Artwork

Kuchotsa Chodetsa Mumpingo; Kufalitsa Uthenga Kopambana Ndi Kuzunzika Kwa Mpingo Ndi Upangiri Wa Gamalieli

1/1/127 minutes, 22 seconds
Episode Artwork

Udani Wa M’chikhalidwe; Kuyendetsa Mpingo Moopa Mulungu; Kukula Kwa Mpingo Muyerusalemu; Ndi Kuona Adani A Stefano

1/1/126 minutes, 26 seconds
Episode Artwork

Kudzikanila Kwa Stefano Pamaso Pa Bwalo La Sanhedrin Ndi Imfa Yake

1/1/126 minutes, 36 seconds
Episode Artwork

Masautso Akulu; Utumiki Wa Filipo; Chikhulupiriro Cha Simoni; Utumiki Wa Petro Ndi Yohane; Mlaliki Filipo

1/1/127 minutes, 4 seconds
Episode Artwork

Filipo Athandiza Mdindo Wa Ku Aitiopiya Kutembenuka Mtima

1/1/128 minutes, 13 seconds
Episode Artwork

Kutembenuka Mtima Kwa Saulo; Utumiki Wa Petro Ku Yopa Ndi Luda

1/1/127 minutes, 10 seconds
Episode Artwork

Chipulumutso Cha A Amitundu Chikudza Ndi Mphamvu Ya Mulungu

1/1/128 minutes, 33 seconds
Episode Artwork

Mau A Petro Odziteteza Pophatikana Ndi Anthu A Amitundu Komanso Tiona Za Mpingo Wa Ku Antiokeya

1/1/128 minutes, 28 seconds
Episode Artwork

Petulo Atuluka Mndende, Paulo Ndi Banaba Abwelera Ku Antiyokeya

1/1/128 minutes, 22 seconds
Episode Artwork

Mulungu Aitana Barnaba Ndi Paulo; Zochitika Ku Kupro; Marko Abwerera Ndi Zochitika Ku Antiokeya

1/1/128 minutes, 34 seconds
Episode Artwork

Uthenga Wabwino Ulalikidwa Ku Ikoniyo, Lustra, Ndi Derbe; Kubwereranso Ku Lustra Ndi Ikoniyo Ndi Antiokeya; Ndi Kubwerera Kunyumba

1/1/129 minutes, 23 seconds
Episode Artwork

Gawo Loyamba La Loona Ngati Mdulidwe Ndi Lamulo La Mose Ndilofunika Kapena Ayi

1/1/127 minutes, 52 seconds
Episode Artwork

Gawo La Chiwiri Loona Ngati M’dulidwe Ndi Lamulo La Mose Ndizofunika Kapena Ayi; Komanso Paulo Ndi Barnaba Apatukana

1/1/128 minutes, 21 seconds
Episode Artwork

Paulo; Kuitanidwa Ku Ulaya Ndi Zochitika Ku Afilipi

1/1/127 minutes, 47 seconds
Episode Artwork

Uthenga Wabwino Ulandiridwa Ku Atesalonika Ndi Ku Berea; Ayuda

1/1/127 minutes
Episode Artwork

Paulo Alalikira Ku Atene Mkati

1/1/128 minutes, 47 seconds
Episode Artwork

Paulo Ku Korinto Ndi Bvuto La Ayuda; Nthawi Pang’ono Ku Aefeso; Ulendo Wachitatu Wa Paulo

1/1/128 minutes, 37 seconds
Episode Artwork

Utumiki Wa Paulo Uchita Bwino Pa Zaka Ziwiri Mu Efeso; Gulu La Oukira Ndimlembi Abwino; Paulo Apita Ku Greece Ndi Ku Korinto

1/1/128 minutes, 10 seconds
Episode Artwork

Utumiki Wa Paulo Ndi Umboni Wake Kwa Akulu Ku Efeso

1/1/128 minutes, 40 seconds
Episode Artwork

Maulendo A Paulo, Zochenjeza Kwa Paulo Ndi Kuti Akhala Ndi A Yuda

1/1/127 minutes, 13 seconds
Episode Artwork

Ulendo Wamasautso Wa Paulo Ku Roma

1/1/128 minutes, 20 seconds
Episode Artwork

Zobvuta Zokonzedwa Ndi A Yuda Zikupitilira Pa Ulendo Wa Paulo Ku Aroma

1/1/127 minutes, 33 seconds
Episode Artwork

Ulendo Woopsa Wa Paulo Ku Roma Ukupitirira

1/1/128 minutes, 18 seconds
Episode Artwork

Ulendo Woopsa Wa Paulo Ku Roma Ukupitilira

1/1/128 minutes, 20 seconds
Episode Artwork

Ulendo Woopsa Wa Paulo Ukupitilira Ndi Umboni Ku Kaisareya

1/1/128 minutes, 58 seconds
Episode Artwork

Masautso A Paulo Akupitilira Pa Ulendo Wake Wa Ku Roma, Kuchitira Umboni Uitanidwa Ku Kaisareya

1/1/127 minutes, 14 seconds
Episode Artwork

Paulo Atsika Ku Kaisareya Ndi Kuyamba Ulendo Wake Wa Pa Nyanja Wopita Ku Roma

1/1/128 minutes, 33 seconds
Episode Artwork

Ulendo Wa Paulo Wamasautso Ukuptilira Panyanja Paoneka Mwera Ndi Kuonongeka Kwa Ngalawa

1/1/127 minutes, 4 seconds
Episode Artwork

Chifundo Cha Anthu Akunja Machilitso Ya Yesu; Ulendo Wotsiriza Ku Roma Ndi Ayuda

1/1/128 minutes, 37 seconds
Episode Artwork

Pemphero La Hana La Ulosi; Ana A Eli Woipa; Mwana Samueli M’kachis

1/1/128 minutes, 38 seconds
Episode Artwork

Kuitanidwa Kwa Samueli; Chilango Cha Mulungu Pa Eli Ndi Ana Ake Chikwanitsidwa; Komanso Chilango Cha Mulungu Pa Afilisti

1/1/126 minutes, 49 seconds
Episode Artwork

Chilango Cha Mulungu Pa Afilisti;

1/1/128 minutes, 35 seconds
Episode Artwork

Sauli Asankhidwa Ndi Kudzozedwa

1/1/126 minutes, 55 seconds
Episode Artwork

Sauli Agonjetsa Amoni Ndi Kuchoka Kwa Udindo Kwa Samueli Kupita Kwa Sauli

1/1/128 minutes, 15 seconds
Episode Artwork

Sauli Apandukira Mulungu; Yonatani Apambana Pankhondo Ya Afilisti; Komanso Kuipa Kwa Lamulo Lofulumira La Sauli

1/1/127 minutes, 7 seconds
Episode Artwork

Kusamvera Kwa Sauli Pa Agagi Ndipo Samueli Mudzudzula

1/1/126 minutes, 55 seconds
Episode Artwork

Davide Adzonzedwa Ndipo Akupha Goliati

1/1/127 minutes, 44 seconds
Episode Artwork

Mulungu Akuphunzitsa Davide; Sauli Afuna Kupha Davide; Ndipo Jonatani Amuthandiza Kuthawa

1/1/127 minutes, 14 seconds
Episode Artwork

Mulungu Alanga Davide; Ndipo Davide Apempha Ansembe Kuti Amuthandize

1/1/126 minutes, 56 seconds
Episode Artwork

Chitetezo Ndi Chisamaliro Cha

1/1/127 minutes, 23 seconds
Episode Artwork

Davide Asonkhanitsa Anyamata

1/1/127 minutes, 28 seconds
Episode Artwork

Davide Akwatira Abigayeli Ndipo Davide Asiya Kupha Sauli Kachiwiri

1/1/128 minutes, 28 seconds
Episode Artwork

Davide Abwerera Kudziko La Afilisti Pamene Sauli Apita Kwa Sing’anga

1/1/128 minutes
Episode Artwork

Moyo Wa Davide Pamene Ali Pakati Pa Afilisti

1/1/127 minutes, 5 seconds
Episode Artwork

Sauli Ndi Jonatani Aphedwa Ku Nkhondo

1/1/126 minutes, 51 seconds
Episode Artwork

Davide Akhazikitsidwa Mfumu

1/1/127 minutes, 13 seconds
Episode Artwork

Davide Akhazikitsidwa Mfumu Wa Israyeli Yense

1/1/126 minutes, 41 seconds
Episode Artwork

Njira Zoyenera Ndi Zolakwika Zomwe Davide Anatenga Pobweretsa Likasa Ku Yerusalemu

1/1/128 minutes, 45 seconds
Episode Artwork

Pangano La Mulungu Pa Kumanga Nyumba Ya Davide

1/1/127 minutes, 42 seconds
Episode Artwork

Ufumu Wa Davide Ukhala Wamphamvu Ndipo Davide Akhala Pa Ubwezi Ndi Mefiboseti

1/1/127 minutes, 45 seconds
Episode Artwork

Davide Ayambana Ndi Ammoni Ndi Asuri Ndi Uchimo Uwiri Waukulu Wa Davide

1/1/128 minutes, 45 seconds
Episode Artwork

Natani Adzudzula Davide Chifukwa Cha Uchimo Wake Ndipo Davide Alapa Chimolo

1/1/127 minutes, 30 seconds
Episode Artwork

Abisalomu Aukira Atate Wake, Davide

1/1/127 minutes, 30 seconds
Episode Artwork

Uchimo Wa Ana A Davide; Amoni Ndi Absalomo

1/1/127 minutes, 14 seconds
Episode Artwork

Za ana aIsrayeli ndi Chikhristu

28 minutes, 58 seconds
Episode Artwork

Mayetsero ena mu chipululu

29 minutes, 4 seconds
Episode Artwork

Ulendo wa pa nyanja yofiira

29 minutes, 25 seconds
Episode Artwork

Chigonjetso ndi mayetsero

29 minutes, 7 seconds
Episode Artwork

Kuchokera ku Egiputo mpaka ku nyanja yofiira

27 minutes, 41 seconds
Episode Artwork

Pasaka, Mlili wakhumi ndi ulendo wa ana a Israyeli

28 minutes, 14 seconds
Episode Artwork

Malangizo a Pasaka

27 minutes, 55 seconds
Episode Artwork

Milili yomaliza

29 minutes, 32 seconds
Episode Artwork

Milili wachiwiri mpaka wachisanu

28 minutes, 55 seconds
Episode Artwork

Milili ina komanso zomwe Farao amakonza

27 minutes, 3 seconds
Episode Artwork

Nkhondo ya Uzimu

29 minutes, 42 seconds
Episode Artwork

Mulungu amuyankha Mose pa zakukhumudwa kwake

27 minutes, 48 seconds
Episode Artwork

Milili yomwe inakonzedwa

29 minutes
Episode Artwork

Kukonzekera muuzimu wa Mose

27 minutes, 3 seconds
Episode Artwork

Kutumidwa kwa Mose ndi zomthandizira zake

28 minutes, 54 seconds
Episode Artwork

Chiyambi Cha Bukhuli, Kubadwa Kwa Samueli

1/1/128 minutes, 1 second
Episode Artwork

Mulungu ayitana Mose

29 minutes, 33 seconds
Episode Artwork

Mulungu akonza mpulumutsi

29 minutes, 50 seconds
Episode Artwork

Malonje abuku la Eksodo

29 minutes, 52 seconds
Episode Artwork

Kupachikidwa kwa Yesu

24 minutes, 49 seconds
Episode Artwork

Imfa ndi kuuka kwa Yesu

25 minutes, 57 seconds
Episode Artwork

Fanizo lomaliza, za Pasaka

23 minutes, 59 seconds
Episode Artwork

Zochitika poyandikira imfa pamtanda

25 minutes, 3 seconds
Episode Artwork

Chizunzo ndi masautso ake

27 minutes, 35 seconds
Episode Artwork

Mafanizo a m'badwo wa mtsogolo poyembekeza

26 minutes, 20 seconds
Episode Artwork

Za masiku otsiliza

26 minutes, 7 seconds
Episode Artwork

Yesu adzudzula akuluakulu achipembedzo komaliza

25 minutes, 11 seconds
Episode Artwork

Yesu atontholetsa akuluakulu achipembedzo

26 minutes, 7 seconds
Episode Artwork

Mau omaliza kwa atsogoloeri achipembedzo

25 minutes, 45 seconds
Episode Artwork

Mfumu iwonetsa njira yakudzichepetsa

23 minutes, 37 seconds
Episode Artwork

Kutsatira mtanda wa Yesu ndi mphoto yake

25 minutes, 48 seconds
Episode Artwork

Kufunika kwa kubadwa kwa tsopano

24 minutes, 33 seconds
Episode Artwork

Banja, kusiyana ukwati ndi ana

23 minutes, 30 seconds
Episode Artwork

Kusanthulika kwa Yesu

28 minutes, 21 seconds
Episode Artwork

Malingaliro atatu a Yesu

27 minutes, 42 seconds
Episode Artwork

Kuyeretsa kwenikweni

24 minutes, 59 seconds
Episode Artwork

Zoonetsa kubwera kwa mavuto

25 minutes, 35 seconds
Episode Artwork

Ufumu wa kumwamba pansi pano

25 minutes, 26 seconds
Episode Artwork

Mafanizo akumwamba

24 minutes, 20 seconds
Episode Artwork

Yesu akangana ndi akuluakulu a chipembedzo

26 minutes, 48 seconds
Episode Artwork

Wofetsa Mbeu

23 minutes, 30 seconds
Episode Artwork

Yesu akhazikitsa ophunzira khumi ndo awiri

25 minutes, 40 seconds
Episode Artwork

Yesu apitiliza utumiki wake

26 minutes, 1 second
Episode Artwork

Yesu apitiliza kuwonetsa mphamvu yake

23 minutes, 58 seconds
Episode Artwork

Zozizwa komanso mphamvu ya Yesu

25 minutes, 6 seconds
Episode Artwork

Yesu kulimbikitsa malamulo

24 minutes, 35 seconds
Episode Artwork

Maubale angwiro

24 minutes, 25 seconds
Episode Artwork

Zammtima ndi zachiyero

24 minutes, 52 seconds
Episode Artwork

Maubale mu ufumu wa Mulungu

23 minutes, 36 seconds
Episode Artwork

Kuyamba chiphunzitso cha pa phiri

24 minutes, 48 seconds
Episode Artwork

Yesus ayamba utumiki wake

23 minutes, 20 seconds
Episode Artwork

Mauneneri ena kukwaniritsidwa

27 minutes
Episode Artwork

Yesu abatizidwa ndi kuyesedwa

26 minutes, 21 seconds
Episode Artwork

Kubadwa kwa Yesu mwa namwali

26 minutes
Episode Artwork

Kukwaniritsidwa kwa uneneri

24 minutes, 41 seconds
Episode Artwork

Mbiri ya makolo a Yesu

24 minutes, 5 seconds
Episode Artwork

Malonje a buku la Mateyu

25 minutes, 32 seconds
Episode Artwork

Madalitso a Yosefe panthawi yomwalira

26 minutes, 41 seconds
Episode Artwork

Mau omaliza komanso imfa ya Yakobo

24 minutes, 45 seconds
Episode Artwork

Yakobo ndi banja lake kwa Farao

25 minutes, 39 seconds
Episode Artwork

Yosefe ayendera Yakobo pa matenda ake

25 minutes, 48 seconds
Episode Artwork

Yosefe aziulura yekha

25 minutes, 53 seconds
Episode Artwork

Yakobo ndi banja lake apita ku Egiputo

26 minutes, 21 seconds
Episode Artwork

Simiyoni atengedwa

23 minutes, 37 seconds
Episode Artwork

Abale a Yosefe afika ku nyumba kwake

25 minutes, 20 seconds
Episode Artwork

Kubadwa kwa Manase ndi Efurayimu

25 minutes, 35 seconds
Episode Artwork

Yosefe atanthauziria malato a Farao

26 minutes, 59 seconds
Episode Artwork

Yosefe atanthauzira maloto

25 minutes, 23 seconds
Episode Artwork

Yosefe alowa mnyumba ya Potifala

26 minutes, 46 seconds
Episode Artwork

Yosefe agulitsidwa kuukapolo

27 minutes, 57 seconds
Episode Artwork

Tchimo la Yuda

27 minutes, 10 seconds
Episode Artwork

Chiyambi cha mkangano kwa Yakobo

26 minutes, 12 seconds
Episode Artwork

Esau achoka ku Kenani kupita ku Phiri la Seya

26 minutes, 40 seconds
Episode Artwork

Yakobo abwerera ku Betele

25 minutes, 6 seconds
Episode Artwork

Dinah adetsedwa ndi Shekemu

25 minutes, 30 seconds
Episode Artwork

Yakono akumana ndi Esau

25 minutes, 25 seconds
Episode Artwork

Mavuto mu wa Yakobo

25 minutes, 48 seconds
Episode Artwork

Mbumba ya Yakobo ndi ana ache

25 minutes, 48 seconds
Episode Artwork

Yakobo athawa ku Halani

24 minutes, 34 seconds
Episode Artwork

Mulungu aonekera kwa Yakobo ku Betele

26 minutes, 25 seconds
Episode Artwork

Yakobo akumana Rakele

25 minutes, 47 seconds
Episode Artwork

Isaki atsimikiza za pangano

26 minutes, 38 seconds
Episode Artwork

Yakobo ndi Rebeka apangana zombera Esau

25 minutes, 31 seconds
Episode Artwork

Imfa ya Abrahamu

26 minutes, 34 seconds
Episode Artwork

Mkazi wa Isaki: Gawo Lachiwiri

26 minutes, 53 seconds
Episode Artwork

Mkazi wa Isaki: Gawo Loyamba

28 minutes, 1 second
Episode Artwork

Imfa ndi kuika mmanda Sara

26 minutes, 22 seconds
Episode Artwork

Mulungu auza Abrahamu kuti apereke Isaki ngati nsembe

27 minutes, 8 seconds
Episode Artwork

Kubadwa kwa Isaki

26 minutes, 56 seconds
Episode Artwork

Abrahamu anamizira za Sara

27 minutes, 21 seconds
Episode Artwork

Mulungu

28 minutes, 24 seconds
Episode Artwork

Hagara athawa

27 minutes, 53 seconds
Episode Artwork

Pangano lamuyaya

27 minutes, 39 seconds
Episode Artwork

Pangano la Mulungu kwa Abrahamu

28 minutes, 2 seconds
Episode Artwork

Abramu apulumutsa Loti

28 minutes, 47 seconds
Episode Artwork

Mulungu aonekera kwa Abramu

26 minutes, 52 seconds
Episode Artwork

Maitanidwe ndi pangano kwa Abramu

26 minutes, 25 seconds
Episode Artwork

Ana a Yafeti, Hamu ndi Shemu

28 minutes, 13 seconds
Episode Artwork

Nsanja ya Babulo

26 minutes, 3 seconds
Episode Artwork

Chimvula chisiya, Nowa atuluka mu ngalawa

27 minutes, 19 seconds
Episode Artwork

Tchimo la Nowa ndi ana ache

26 minutes, 28 seconds
Episode Artwork

Malangizo kwa Nowa pa Chingalawa

27 minutes, 50 seconds
Episode Artwork

Kuunika Mbiri ya Enoke

27 minutes, 33 seconds
Episode Artwork

Mulungu apereka mwai wachiwiri

27 minutes, 3 seconds
Episode Artwork

Chikonzero cha Mulungu Chamtsogolo ndi chipulumutso

26 minutes, 14 seconds
Episode Artwork

Tchimo la Munthu

26 minutes, 17 seconds
Episode Artwork

Kulenga Munthu

27 minutes, 39 seconds
Episode Artwork

Kulenga Dziko Lapansi

26 minutes, 43 seconds
Episode Artwork

Chilengedwe cha munthu

27 minutes, 35 seconds
Episode Artwork

Chiyambi cha Dziko

26 minutes, 3 seconds
Episode Artwork

Kumvera Mau

25 minutes, 54 seconds
Episode Artwork

Baibulo lichokera kwa Mulungu

27 minutes, 23 seconds
Episode Artwork

Maziko a bukhu la Genezesi Gawo Loyamba

27 minutes, 3 seconds
Episode Artwork

Maziko a bukhu la Genezesi

27 minutes, 28 seconds
Episode Artwork

Kusanthula Baibulo

27 minutes, 17 seconds
Episode Artwork

Kulingalira pa Mau

26 minutes, 2 seconds
Episode Artwork

Kuwerenga Baibulo

28 minutes, 48 seconds
Episode Artwork

Powerenga Mau yambani ndi pemphero

29 minutes, 55 seconds
Episode Artwork

Kufunika kwa mau otsogolera

28 minutes, 46 seconds
Episode Artwork

Kufunika kwa Baibulo

28 minutes, 26 seconds
Episode Artwork

Kuwauza ena za Baibulo

26 minutes, 37 seconds
Episode Artwork

Kuwerenga zomwe ena analemba

27 minutes, 29 seconds